Pa 10 October 2015, dziko la Malawi likhala likukondweleranawo tsikulo kumbikira chisamaliro kwaodwala matendaokhalitsa pa dziko lonse. Mutu wa ukulu chaka chino ndi: “OdwalaObisika, UmoyoObisika”
Ili ndi tsiku lomwe linakhazikitsidwa kuti tonse tidzilingalira ndikusangalira ntchito yopereka chisamaliro kwa odwala matendao khalitsa pa dziko lonse. Tsiku lilimaperekanso mwayi odziwitsa anthu kuti amvetse bwino za nkhaniyi komanso kutitipeze thandizolo gwirira ntchitoyi kuti iyende bwino.
Chikondwelerochi, chomwechidzakhalepo Loweruka pa 10 September 2015 kuyambira 9:00 koloko mmawa, chidza thandiza kuonjezera mwaioti odwala matenda okhalitsa makamaka omwe alima loobisikamonga kundendeya Maulakomanso kumalo a asirikali a Kobe Barracks ku Zomba athandizidwe.
Mutuwachakachinowu;“OdwalaObisika, Umoyo Obisika” ukukolezera chidwikutitiganizire onse omwe akudwala matendao khalitsa ndi poakukhala kumaloomwe amavutika kutiapeze thandizo ndichisamaliro choyenera.
Bungwe la Zaumuoyo pa dzikolonse la WHO linapeza kuti m’modzi mwa anthu 100 aliwonse amasoweka chisamaliro cha odwala matendaokhalitsa. Ena mwaodwala amene wandianao mwenthawizambiri amai walikandipo amabisika. Tikamanena zopereka chisamaliro kwa odwala matendao khalitsa, aliyense ndi ofunika ndi po aliyense ayenera kulandira chisamaliro chi.
Tsikulilidzathandiza nsokubweretsa pa modzi akuluakuluo konza malamulo antchito yikomanso mabungwe otithandiza pachituku kondiothandiza popereka chisamalirochi kwa odwala ngati gulu limodzi lacholinga chimodzi. Unduna wa za umoyomo gwirizana ndi Bungwe la Palliative Care Association of Malawi akukuitanani nonse kumwambowu.
Mac Phail Magwira PhD
MLEMBI WAMKULU MU UNDUNA WA ZAUMOYO
Undunawa Zaumoyo